MASALIMO. 117. Tamandani Yehova, inu anthu a mitundu yonse; mulemekezeni Iye, inu mitundu ya anthu. Pakuti chikondi chake pa ife ndi chachikulu, ndipo kukhulupirika kwa Yehova nʼkosatha. Tamandani Yehova.